................. On a serious note Koma sonotu ma feminist - TopicsExpress



          

................. On a serious note Koma sonotu ma feminist movement achuluka Malawi muno.. Nafe tibweletsa yanthu coz women also do manipulate men amwene..... Zoona amachita kuwelengela ma-pad(condoms/chitetezo) akabwela kuti atsalapo angati... Ikasowa nkhondo amwene wapanga nayo chani n ndindani... Kodi mwati ngati nyamata zawo wapenza kuti ajozy tigayileni mapad atsapatsidwe..... Asaaaa manipulation ipotse apa #fotseki lolest... #BRING_BACK_FREEDOM
Posted on: Mon, 14 Jul 2014 08:05:49 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015