A Football association of malawi alephera kuyendesa mpira mmalawi - TopicsExpress



          

A Football association of malawi alephera kuyendesa mpira mmalawi muno ndipo angosiyira anzawo ayesepo.Nthawi ija kamuzu stadium itatsekedwa mesa a Fam ankakana kutsegula ankati alibe mphamvu,lero atseka bwanji stadium ndipo mphamvu azitenga kuti?.Wandererz idamenyedwa ku chitowe,stadium anatseka?,masapota a bullets adamenyedwa ku Dedza Gomezgani zakazaka naye anali konko,koma stadium anatseka? Nanga osewera wamenya bolera uja amutani poti mwanayo pano ali ku ICU?.Anthuwa angovomela kuti ntchito yawakanika ndipo alibe mphamvu yotseka stadium.Ife ngati masapota tikumana ndipo tikambirana zomwe titachite koma mukuwona kwanga siikhala yotseka mpaka masabata atatu,watero Mabvuto Chiwambo yemwe ndi wa pampando wa masapota okhudzidwa ku Blantyre.....@Namzy
Posted on: Tue, 15 Oct 2013 05:20:57 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015