AMBUYE MULUNGU DALITSANI ATUPELE PINCODE MULUZI, NYAMATAYU CHAKA - TopicsExpress



          

AMBUYE MULUNGU DALITSANI ATUPELE PINCODE MULUZI, NYAMATAYU CHAKA CHA MAWA MENE AKUTENGA BOMA AZAKHALA NDI CHINTCHITO CHACHIKULU Bwana wolemekezeka Hon Atupele Pincode Muluzi chaka cha mawa2014 pamene mukutenga boma muzakhala ndi chintchito chachikulu, (1) njala ku malawi ndiye ilipo ya mnanu moti chimanga chachoka pa k2500 panopa chafika k15,000 (2) bwana kukuyalidwatu miyalatu ya maziko, ndiye muzakhala ndi chi ntchito chomanga monsemu , koma mmmhhhh yayalidwatu yambiri madera ambiri eish muli ndi chintchito moti nduna yanu ya ntchito izalimbetu, malekano monsemu akuyalamo miyala ya madziko moti ikanakhala mijigo ya madzi bwezi tikuti mabvuto amadzi achepa mdziko muno,
Posted on: Fri, 30 Aug 2013 19:50:22 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015