ASodzi asowera mnyanja!!! asodzi asanu omwe ndi pachibale, - TopicsExpress



          

ASodzi asowera mnyanja!!! asodzi asanu omwe ndi pachibale, onse mayi mmodzi bambo mmodzi kunkhotakota asowa mnyanja ya malawi lachinayi sabata latha.Asodziwa odapita kokatchera makombe ophera nsomba ndipo odakwera boti koma mwatsoka mpaka pano sodabweleko.mchimwene wawo wosodziwa ni yemwe adadabwa kuwona kuti obale ake solubwelako.ndipo mpaka pano sodatulukire.asodziwa ndi a zaka za pakati pa 18- 35.MNENELI Wa police ku nkhotakota wati kufufuza kuli mkati.ozanga onse umira pachibale.olira bwanji? Kk
Posted on: Mon, 22 Jul 2013 02:51:24 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015