Admin tabisa dzina langa utumize aka.achinyamata amasiku ano - TopicsExpress



          

Admin tabisa dzina langa utumize aka.achinyamata amasiku ano sazakapulumuka kumwamba ndi tchimo lonama eeeeshiii!..mwaonjeza,amvekere ndili ku limbe pa foni chonsecho ali nyumba.,kufunsira kapena kufunsilidwa umva sindili pabanja chonsecho wasiya mkazi kapena mwamuna.umva i love u so mutch ali ndiuyu akapita kwa uyonso i love u so much,weniweni umukonda ndiuti kaya,kwinako malizisani nokha ukhuluku mumapangawo..koma musinthe..
Posted on: Fri, 16 Aug 2013 04:20:58 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015