Afta sucsesfully tym with chikondi stopover this iz what i paid - TopicsExpress



          

Afta sucsesfully tym with chikondi stopover this iz what i paid Dissimisal.the man so called Daniel Malenga.what a man why so jealosy with me chinakuwawa ndi chani kuti undi khomelele remember chuma chija sichako olo undikhomelele chichako.ukanakhala wanzelu bwezi ukusova mavuto ako osati kukokela chibale.wandichosetsa ntchito mulungu watsegula khomo lina ingolinda madzi uziona,munthu wankulu koma jerus losayamba uzipanga zako osati zaine,konzani mavuto anu osati mupange zaine.nde ukanangolimbika ntchito osati kundilonda londa.chuma chija sichako. Thanks sales line for re emproyee me.thanks chikondi makadali for gud tyme,thanks bouncer,mastern,feleni for gud company.thanks mrs makadali for careling and love u shown me. Wishing all the best 2 management end the entir staff.once again thanks salesline.nde sunati uziona.
Posted on: Sun, 30 Jun 2013 16:37:42 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015