Akuti Waiponda galimoto fyuuuu! akuyendera 80 malo a 50 speed - TopicsExpress



          

Akuti Waiponda galimoto fyuuuu! akuyendera 80 malo a 50 speed limit. Wa speed trap nkudzaimitsa galimoto. waspeed trap: takugwirani. Oyendetsa. Ndalakwanji? Waspeed limit.mwachita exceed speed limit, simunaone chikwangwani cha 50? Oyendetsa: ndachiona cha 50, koma 50 ndi chani? Height, width, length kapena chani? Ine ndaona chikwangwani cha 50 osati 50km/h. Nde mukalembeponso km/h. #inu muli Waspeed trap mungatani?#
Posted on: Tue, 04 Nov 2014 14:38:39 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015