Anthu ambiri pafb pano mumaona ngati malo opangila matama, - TopicsExpress



          

Anthu ambiri pafb pano mumaona ngati malo opangila matama, makamaka inuyo agongoli achitsikananu, basi busy kumapanga update info. ku profile yanu kuti you Live in Gautenberg, RSA, ena mumvekele, Hawton, UK... Ayi ine ndimakhala ku Ireland... Chonsecho ndinu akapoli achabechabe mukungotuwa ndi fumbi kusoche kwamanje enanu Kwamgona kulcity... Kwamanje, kumachinjiri, kwamgona, ku25 kwasanduka liti ku Jon??? Mxiew, zitheretu mwamva magututu amabodza inu??? Ndikadzangokuzindikila kuti wapanga update info yabodza kuprofile yako, ndidzakuthidzimula chimbama cha amai inu mundipondela mwana... #2kay [[chelseafc]]
Posted on: Sun, 20 Oct 2013 18:28:53 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015