Apa ndemwatiuza kuti Joyce Banda sanabenawo ndalama mboma nde bwanji inu anthu a DPP mnali kumnyoza mai wabwinoyi?Kuyambira MCP :UDF;DPP mnaba mboma komanso simnali kufufuza nkhani koma Joice Banda watsonyeza kuti ndimnthu okonda Malawi ataona ndalama zaboma zikutha anaitanitsa anthu Ofufuza inu a Dpp mpaka lero mkulephera kufufuza 92 billion mnaba ija.Kuyambira lero msazamnenenso Joyce Banda chifukwa ndi President yekha watsonyeza umunthu Cashgate mnali kuinena ija sikumkhuza komanso sanaphepo mnthu
Posted on: Fri, 31 Oct 2014 04:18:59 +0000