Austin anamuwuza kuti ayankhule kwa a president mmalo mwa mp. - TopicsExpress



          

Austin anamuwuza kuti ayankhule kwa a president mmalo mwa mp. Tsono iye anazowera chiyankhulo chakwawo koma anamuwuza alankhule chichewa Austin. Bwana ife kuno takulandilani toze. Ndipo tikukutokosani kwambiri. Potimangira bulizi (bridge) koma chiwolo (holo) chachikulu.bwana muzaziye mtima umenewu Kodi Austin anali wa chiyankhulo chanji? A. Sena B. Chichewa C. Chiyao D. Tumbuka E. Tonga Milly
Posted on: Mon, 02 Sep 2013 20:09:25 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015