BIG BULLETS IPEREKA 5N YA K100,000 Mlembi wamkulu wa SULOM - TopicsExpress



          

BIG BULLETS IPEREKA 5N YA K100,000 Mlembi wamkulu wa SULOM Williams Banda wati team ya Big Bullets ilipira 5n ya K100,000 pazomwe yachta dzulo team yi ku nchalo, team ya bb inalembesa ku sulom kut ikapita koenda izimenyera jenz ya white ndipo pakhomo azimenyera ya red, pamene team ya BT UTD inalembesa kut pakhomo Azivala jenz ya white pamene koyenda azivala ya red, koma dzulo zinapezeka kut ma team onsewa anavala jenz ya red ndipo a BB anakabwereka jenz ya nchalo united yomwe sili mu superleague #LICKY_1...
Posted on: Sun, 24 Nov 2013 05:38:38 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015