BOMA ili tilibe nalo mawu mwezi iwiri osalipidwa tilindi ngongole - TopicsExpress



          

BOMA ili tilibe nalo mawu mwezi iwiri osalipidwa tilindi ngongole za anthu chifukwa tikamabweleka ndalama timawauza kuti tilandila mwezi wa mawa Koma mpaka lero sitikulundila, WATERO phunzitsi wa #Zingwangwa primary sitikupita Ku ntchito mpaka boma litatipasa ndalama zathu. #MWAANA Omwe aliokhudzidwa aseka misewu ya #Zingwangwa pokhunzidwa ndimene akumvela,kodi mufuna tisaphunzire watero mwana wa Ku Chimwakhunda primary pokwiya uku akuseka mseu wa zingwangwa via chilobwe. #mkeki
Posted on: Wed, 19 Nov 2014 15:00:41 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015