Bengo kusanzikanandi mkazake paulendo wake okaona anthu kumudzi: - TopicsExpress



          

Bengo kusanzikanandi mkazake paulendo wake okaona anthu kumudzi: Bengo: sweet basitu ine ndikupita ulendo wakumudzi kuja musale bwino. mkazi: mwatenga zofunikra nzonse?. Bengo: yeah ndatenga. Mkazi:nanga ma condom mwatenga? Bengo: darling achani popeza inu simupit nawo? Mkazi: mwangozi zimatha kuchitika ndikuwafunatu. Bengo:yeah zoona basi ndiyikileni nchikwama. Mkazi: nane mundisiyile awiri anga. Bengo: chifukwa? Mkazi: nane ndikupangila mwangozi zitachitika nditha kuwafuna. Bengo: basi sindipita ulendowu ukhala ndi minyama. mau amodzi kwa Bengo #chindinho
Posted on: Tue, 19 Aug 2014 17:58:54 +0000

Trending Topics



La segunda fecha del futsal oficial, organizado por la Liga de
Sentimentele unei femei nu pot fi măsurate pe jumătate. Femeia
Topics Afghanistan Al Qaeda Building 7 Bush Administration CIA CNN
Hope you all had a good Good Friday. We have some more CDs and
#LSS When you’re alone and life is making you lonely You can
One more thing. As the folks talk about the murdered animal, lets

Recently Viewed Topics




© 2015