Binoni Anyamata osapyolera makumi awiri agwidwa ku binoni pomwe - TopicsExpress



          

Binoni Anyamata osapyolera makumi awiri agwidwa ku binoni pomwe amakapangitsa ma clearance kuti athe kukhala ndi ma work permit a original. Anyamatawa atamva nkhani ya ma work permit kumayambiliro adanyalanyaza koma amnzawo atawauza ndipomwe amapita nawo.Tsoka ilo ambiri adaiwala kuti adaika ma permit wokonzedwa ndi a home affairs achimalawi.Atawonetsa chiphaso amangoikidwa kumbali pamapeto ake angowatenga wa ku lindela. Durban Ana atatu amwalira atagwidwa ndi nyesi ya mphamvu za magetsi.Anawa akuti amathamangira makolo awo omwe adali mu chigulu chopanga strike kuti boma iwayikire magetsi mnyumba zawo. More news!!.. #advisor02
Posted on: Thu, 09 Oct 2014 08:02:46 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015