CHINKHOSWE CHINKHOSWE RICHARD AND DINNAH Katswiri wotseka pagolo - TopicsExpress



          

CHINKHOSWE CHINKHOSWE RICHARD AND DINNAH Katswiri wotseka pagolo komanso Captain wa team ya Be Forward Wanderers Richard Chipuwa mawa laliwisili pa 26 Dec 2014 akhara akupanga chinkhoswe ndi Dinnah Chizinga mu mzinda wa Blantyre. Poyankhura ndi MSLNSF Richard wati iye ndiwokondwa kwambiri chifukwa ichi ndi chiyambi chokwaniritsa malingaliro anga wofuna kumutenga Dinnah ngati mkazi wanga. Richard wati zonse zikachitikira ku Kings Garden (opposite Blantyre post office) kuyambira nthawi ya 1 Oclock.
Posted on: Thu, 25 Dec 2014 19:36:35 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015