Chauta atakuwuza lero kuti:mwana wanga ndimakondwela ndi ntchito - TopicsExpress



          

Chauta atakuwuza lero kuti:mwana wanga ndimakondwela ndi ntchito zako zabwino pachifukwa chimenechi ndakupatsa mwayi oti usankhe munthu mmodzi mwa awa kuti adzakhale limodzi ndi iwe kumwamba kuno ukadzamwalira ungasankhe ndani mwa awa: 1. Mkazi wako 2. Mwamuna wako 3. Ex wako 4. Girlfriend wako 5. Boyfriend wako 6. Amayi ako 7. Abambo ako 8. Aunt ako 9. Uncle ako 10. Daughter wako 11. Mwana wako(son) 12. A neighbour ako 13. Others specify K£rnel The
Posted on: Wed, 09 Jul 2014 16:23:30 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015