Chimwemwe>guys ndatenga mimba koma guy yathawira ku joni pamenepa - TopicsExpress



          

Chimwemwe>guys ndatenga mimba koma guy yathawira ku joni pamenepa ndipange bwanji? Ndazindikira dzulo pomwe ndinamufusa nzake akundiuza kuti basi amene uja waotcha ntambo vuto pano ndiloti kwathu sangandisunge ngati amve zimenezi ndipo nzake wa boyfrnd wangayu wandipempha kuti bwanji asamale mimbayi? Kodi pamenepa ndilore watiso nditha kukamutchula kwathu ati wakhala akundifuna mwina umenewu ndimwayi wake mukuti bwanji guys? Ndimuvomere?
Posted on: Fri, 29 Nov 2013 04:42:41 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015