Copy & pasted Mwachidule zatha chonchi ku state house: Reporter: - TopicsExpress



          

Copy & pasted Mwachidule zatha chonchi ku state house: Reporter: What do you kno about the KCH mortuary? JB: Ine sindikuzidziwa Reporter: Tell us about the sell of the jet? JB: Sindikudziwaponso kanthu, tawafunseni awowo. Reporter: Tell us your wealth JB: Ine ayi zimenezo go and speak to the speaker of the national assembly. Reporter: What is the stand on the lake dispute with Tanzania? JB: Achimwene sindikudziwansotu kanthu ine zimenezo, a chiume tayankhanipo. Reporter: Kodi nkhani ya mayina mu forensic audit ikuti bwanji? JB: Ine ndikungomvanso anthu mukukamba sindinayiwelenge nkomwe koma azungu akuti atiwuza chochita akubwela posachedwapa. Mawu anu omaliza a president. JB: ine ndikungofuna kudziwa za K96 Billion ija basi kuti inapita kuti. Zikomo
Posted on: Tue, 04 Mar 2014 19:25:05 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015