Deborah> mayi anga andilanda boyfrnd wanga yemwe ndi mphuzitsi - TopicsExpress



          

Deborah> mayi anga andilanda boyfrnd wanga yemwe ndi mphuzitsi wanganso chibwezi chawo chidayamba pomwe aphuzitsi anayitanisa makolo keno eti mpaka mayi anga kugwa mchikondi ndi aphuzitsi angawo zikumandiwawa akabwera kuzagona kunyumba kumachindana kuchipinda ine ndekha kuchipindakwanga guys m tired I think siten yangayi have gone too far ndiye ndahganiza zoti ndingoyimwetsa tameck kapena accid mwina guy yangayi indikwatiraa sindingalore kuti ine ndi mayi anga tizi share rana mwamuna mmmmh guys thandizeni b4 I du sm tin stupd
Posted on: Thu, 24 Oct 2013 11:48:35 +0000

Recently Viewed Topics




© 2015