EBORA WAPOSA HIV AIDS IWE. - TopicsExpress



          

EBORA WAPOSA HIV AIDS IWE. MAYOO! MAYOO! INE, NDAFA BASI!. Ha! Iwe Ebora,watiwonjeza zedi. Maso anga aja, thupi langa lija,mutu wanga uja, Ha! Ka Virus ka Ebora kapwetedza. Mmimba mwanga muja mwayamba kutsegula mosalekeza ngati wina akujinga Jingo.Kuchimbuzi ndikumathako 5 hours, ha! Ndafa ine basi. Zizindikilo zako Ebora ndi izi: Kutsegula mmimba mosalekeza, Kuphwanya thupi lonse,Mutu umabandula kwambiri,Kutopa kwambiri,Kusamza kosalekeza,Thupi limasinthirako pangono kumkerako kokuda,Thupi limafowoka kwambiri, Zilonda pakhungu, kuzizidwa kwa thupi, Kukhosomola kosalekeza,komanso kuwonda. Komanso Mtembo wamunthu wa Ebora sugwiridwa ndi Manja.kungoti wagwira,basi nawenso watenga Matenda a Ebora.komanso matendawa akakugwira, Munthu sumachedwa kufa. Ndipo 2 days simatha iwe usanafe. Ebora ilibe Mankwala ndiponso sichizika. Nthendayi inachokera ku Nyani komanso Muleme. Njira zotengera Ebora ndi izi : Kukhudzana , Kupumilana mpweya, kukhudza masamzi, kudyana milomo,kuvalilana zovala komanso kupatsana moni.Ndipo munthu wodwala nthenda ya Ebora; Sitigona naye pamodzi. Ayenera kusalidwa ngati munthu wodwala matenda Akhate. Matendawa kuno ku Malawi sanafike.Koma mayiko akunja ngati: Sierraleone ,Guinea,Mali komanso ku Nigeria sanafale kwambiri. Abale ndi Alongo tiyeni tizipemphera kolimba kuti Ebora isafike mudziko lathu lino la Malawi.Komanso tiyeni tilape machimo athu kuti Mulungu wakumwamba atikhululukire machimo athu.Milili ya matenda ndipo sidati ,pakuti izi zadza chifukwa cha Uchimo wathu. Anthu ambiri lero amukana YEHOVAH koma Satana naye kakaka!. Satana kwake ndikupha ndikuwononga basi. Zunguliro Phwatha, YEHOVAH IFE TIDALIRA INU NDIPO TIWOMBORENI KU MULILI UMENEWU. Ebora kills faster than HIV AIDS.
Posted on: Tue, 19 Aug 2014 18:13:43 +0000

Trending Topics



ght:30px;"> Cancro: in USA si studia il bicarbonato, In Italia Simoncini è
On this day (Oct. 1) in 2007: Radioheads official website crashed
Despite its oppressive and brutal history, Mr. Assad’s regime
The mystic aura of India and the enigma that she is has captured
Australian renewable energy boosts local economies through a range

Recently Viewed Topics




© 2015