Fyn... Last wkend ndinapita ku lilongwe kwa ma hope anga kukacheza - TopicsExpress



          

Fyn... Last wkend ndinapita ku lilongwe kwa ma hope anga kukacheza ndye ine fon zanga sindinazibise ndinazisiya pa mpando ine ndinali panja mwamuna uja anatenga fon zanga zija ndikumaona ma pixturez anga ndi ku lowa pa fb ku account yanga koma iyeyo anapeza ku ma pix kuja kuli ma pixturez ambiri amwana yemwe ali wa brother wanga... Koma iye sanandifunse pompo kut uyu ndi ndani mpaka ndinabwelako... dzulo wangolemba message kut chicco ali bwanji? mining mwana uja... kenako anvekele ndinakukonda koma ndaona kut uli ndi mwana ndye basi ndasintha maganizo, yet ine ndilibe mwana ndamuuza kuti mwanayo ndi wa bro wanga koma izi sizikunveka ndye ine nditani????
Posted on: Fri, 04 Oct 2013 07:25:52 +0000

Trending Topics



/b>
Attention KAUAI! I’m sorry to announce this Friday night “So
በአባይ ጉዳይ ሱዳን ከግብፅ የተለየ
✖ Interior Accessories Coverking Center 50/50 Bucket Custom Fit
A noo artikle calt Ashton Kutcher and Mila Kunis Have an Elaborate

Recently Viewed Topics




© 2015