Greatest and wisest pipo of our land how are u doing? I am doing - TopicsExpress



          

Greatest and wisest pipo of our land how are u doing? I am doing great ine. Lero... Ine ndakhala mu relationship ndimamuna wanga for 2 yrs, anandipatsa mimba pano mwanayo is a yr and some months old. Zaka zonsezi osadziwa kuti boyfriend wanga is married and has kids. I am 20 iyeyo is 31. Ndimakagona kwao osadziwa kuti sikunyumba kwake kweni kweni koma nkwa brother wake yemwe ali ku US. Ndimatha kukakhala wk kwathu ndimawauza kuti ndapita kwao kwa mnzanga wa ku school. Mnzanga wina wandiuza a wk ago kuti anakumana ndi boyfrnd wanga ali ndi mkazi ndi ana ku Mangochi pa 6 Juy, ndinamufunsa ndipo sanakane anavomera akuti amaopa kundiuza kuti ndimukana komanso nditha kuthetsa relationship yathu. Now that I know the truth sindikudziwano chochita. Iyeyo wangondiuza kuti ganiza undiuza zoti tichite. Gud pipo ndithandizeni chonde nditani?
Posted on: Wed, 23 Jul 2014 07:09:24 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015