Guyz kalembera wa chisankho akhala ali kumachinga kuno - TopicsExpress



          

Guyz kalembera wa chisankho akhala ali kumachinga kuno posachedwapa tiyeni amene takwanitsa,amene tizakwanitse zaka 18 tsiku lovota lisanakwane tikalembetse,,,,Kalemberayu ndiwathu ife tili nzika ya malawi....Tisaiwale kuti mwaiwu umabwera kamodzi pazaka zisanu .Kalemberayu ndiosankha patatu:Nkhasala wawodi yathu, Mp wadera lathu komanso pulezidenti wadziko...Tikapanda kulembetsa nditizapeza mwai wovota tizapatsa pata amene sitikumufunayo..Voti yanu ndiufulu,ndikusankha kwanu.Uthengawu akukupatsirani ndi a MEC.
Posted on: Wed, 04 Sep 2013 21:19:13 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics



1.

© 2015