HEHE ZOVUTA KWABASI. ZIMVERE MTOLOMO Kafukufuku wasonyeza kuti - TopicsExpress



          

HEHE ZOVUTA KWABASI. ZIMVERE MTOLOMO Kafukufuku wasonyeza kuti amuna/akazi amene amadzifaila/kupaka perfume samatero ngati mwa manyado ayi,koma amakhala kuti afuna aphe ka fungo kooipa komwe iwo amatulutsa kaya ku mnkhwapa,mkamwa komanso ku chikangawaku(private part). Azibambo ndiye sasamba amangomenya surmary kusukusula,then amangozipaka perfume. Izii zodzoladzolazi kwambiri amazikonda kwambiri ndi atsikana ndi azimayi ngatitu anapanga za decolation and body painting. Akaziwa malo akapaka perfume malo moti azinunkhira ndi pameneno amanunkhano coz mopakidwa mumachuluka. Handbag ya munthu wa mayi ikanakhala shop bwenzi ili yosasowa katundu,iwo dzala amapaka cuttex fungo lakelake,tsitsi/weave amalithira perfume fungo lakelake,kunkhwapa amathirako perfume fungo lake lake,mphechepechemu amadzodzamo powder fungo lake lake,nkhope amaidzodza mafuta akeake thupi nalo limalowa mafuta akeake,zikope zimathilidwa mafuta akeake,milomo amathwanimisa ndi timafuta taketakenso koma totchipa ngati ito,mu Limbe mu ndi K50 koma iwo amanama anagula ku Joni. Hehe zovu zedi ndithu. #Village_Monger
Posted on: Thu, 12 Sep 2013 10:19:27 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015