Haha ameneyo ndiye munthu zikamapanda kukuyendera amafatsa - TopicsExpress



          

Haha ameneyo ndiye munthu zikamapanda kukuyendera amafatsa mkumakunena kuti ndiwe waulesi,wopusa,opanda nzeru,osalimbikira,osathandiza,osaoneka bwina komaso obadwira banja losauka choncho sungachite bwino koma zikayamba kukuyendera amasitha mkumati ndiwe wamatama,odzikonda,okhwima ,okuba,ndiwe gay chifukwa chodzisamalira and every1 turn 2 be a relative even omwe chinatha.This is just the bignin watch second step
Posted on: Sat, 23 Aug 2014 11:44:58 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015