Hide my identity Nthawi ina yake ndinali ndikucheza ndi - TopicsExpress



          

Hide my identity Nthawi ina yake ndinali ndikucheza ndi girlfriend wanga munyumba ya myamata mzanga,mwadzidzidzi kunatulukila mayi ake ndikugogoda chitseko.Nditatsekula adalowa ndikutengamo mwana wawoyo koma akukalipa kwambili mpaka kufuna kumumenya.kuchokela tsiku limenelo mpaka lero ndisadacheze nayeso mkaziyu bcoz next day yake idali yoti ine ndizivaya kuno ku xool.kodi pamenepa mkaziyi ndingomusiya kapena ndipitilile naye mchikondi?
Posted on: Sat, 28 Sep 2013 11:55:09 +0000

Trending Topics



P P Y B I R T H D A Y to a person that he is not only my

Recently Viewed Topics




© 2015