#JAME Jame anamwalira ndipo atafa anapita ku jahena..kunenekuja - TopicsExpress



          

#JAME Jame anamwalira ndipo atafa anapita ku jahena..kunenekuja anakapeza Queen Elizabeth waku england ndi George bush.. Anamupeza satana akutchaja foni yake chifukwa Queen ndi George amafuna ayimbe phone kwao kuti amve kuti anthu alibwanji. Queen anayimba foni kwa 5minutes ndipo atamufunsa satana kuti ndalama zakwana zingati anati zakwana $5000 kenakonso george anayimba kwa 30minutes ndipo anauzidwa kuti apeleke $10 000 Naye #Jame anafuna ayimbe phone ku #Malawi kuti amve momwe dziko likuyendera..Anayankhula ka #1hour ndipo satana anamuuza kuti apeleke #K50 apa jame anadabwa kuti call yake yatchipa cifukwa chani Atamufunsa satana cifukwa call yake yatchipila kuposa enawo .satana anati "ukudziwa kuno ndiku jahena.ndie kuyimba kumalawi ndikotchipa chifukwa kumalawinso ndiku Jahena zilingati kuimba Local call.. Admin+18
Posted on: Sat, 21 Sep 2013 08:27:49 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015