JB Akuopa Kubwera Kuno Kumalawi Pankhani Ya Cashgate,akuti - TopicsExpress



          

JB Akuopa Kubwera Kuno Kumalawi Pankhani Ya Cashgate,akuti Akabwera Kuno Adzamangidwa,kodi Pamenepa Tinene Kuti Iyeyu Dzikoli Amalifunira Zabwino?Kodi Misonkho Yaanthu Osauka Wina Ndikuitenga Kukalemba Pa Will Yake Ndizoona?Panopa Prof Akuvutika Kubwezeretsa Chuma Pamodzi Ndi Financial Minister Goodal Chifukwa Cha Satanist JB,amalawi Anzanga Plz Tisamangoombera Satana Mmanja Pazinthu Zoononga Dziko.Anthuwa Amaona Kuti Presidential Post Pali Bwemba Thus Why Achakwera Anasiya Kutumikira Mulungu Ndikutsa Zacaesala.Tisamanazidwe Ndizinthu Zochepa Koma Tiyangane Tsogolo Ladziko.Ndimasilira Botswana,simapempha.I Support Zero Aid Budget!
Posted on: Thu, 15 Jan 2015 16:59:47 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015