Jessie mlhakho Kaliati Admin ndipangireni post pliz.ndine - TopicsExpress



          

Jessie mlhakho Kaliati Admin ndipangireni post pliz.ndine wosangalala kwambiri kamba koti nkhani yokhuza Ellen ndi Mesho yabwera poyera.Ine zimandibowa kwambiri chifukwa choti Mesho ndimamupoyilira koma sanali nane ndi ntchito.Nde ndasangalala kwambiri chifukwa choti uhule wa anthuwa waonekera pachulu.Bill ya maphone yimakwera mwezi ulionse chifukwa cha awiriwa.each and every time amangoyimbirana pa ma phone amu office.ndiye atsikana anzanga tengeranipo phunziro.sibwino kumayenda ndi mwamuna wa eni mix wapa banja.Si izi tsono! Wayalukatu Ellen!!! Malawi yonse kudziwa kuti amayenda ndi Sugardadie!! Ngati mkufuna mudziwe zambiri zokhuza Mesho ndi Ellen pitani ku Nyasatimes fb page muona. #PDK
Posted on: Fri, 10 Oct 2014 19:23:12 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015