KODI MUKUDZIWA -Antarctica ndi continenti yokhayo padziko lapansi - TopicsExpress



          

KODI MUKUDZIWA -Antarctica ndi continenti yokhayo padziko lapansi komwe sikupezeka njoka. -Munthu amalota pafupifupi ka 1,460 pa chaka. -Pa chaka munthu amadya chakudya chokwana pafupifupi makilogalamu 27,215,chimene chikufanana ndi kulemera kwa njovu 6. -Amuna 58 pa 100 amene adalekana ndi akazi awo amanena kuti akusangalala tsopano. -Kuwawa kwa tsabola sizimatengera maonekedwe ake koma kuchepa kwake.Tsabola wangono amakhala wowawa kwambiri kusiyana ndi wamkulu kwambiri. -Europe ndi continenti yokhayo yomwe kulibe chipalamba(desert #Goodnight pammawa tizachezaso bwino #chindinho
Posted on: Thu, 04 Dec 2014 21:54:30 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015