KOMA KASAMBARA SINDIKUFUNA ZOYAMBANA WAMVA? - JB. Mtsogoleri - TopicsExpress



          

KOMA KASAMBARA SINDIKUFUNA ZOYAMBANA WAMVA? - JB. Mtsogoleri wadziko lino mayi Joyce Banda wati zimene akuchita Raph Kasambara yemwe anali nduna yazachilungamo ndizodandawulitsa kwambiri. Mayi Banda ati, Kasambara ndi amene akumamutuma Pika Manondo kuti azimunamizira iye kuti ndiamene anamutuma kuti awombere a Paul Mphwiyo zomwe malingana ndi mayi Banda ndizongofuna kuwayipitsira dzina lawo. Kotero mtsogoleriyu wachenjeza Kasambara kuti zimene akuchitazo akapitiliza awona mbwaza. #Linda wa #Bnm.
Posted on: Thu, 07 Nov 2013 20:23:33 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015