KUFUKULA NKHAZA ZINA ZOMWE ZIMACHITIKA MU NTHAWI YA - TopicsExpress



          

KUFUKULA NKHAZA ZINA ZOMWE ZIMACHITIKA MU NTHAWI YA MCP!!!! 1.Ukakhala kuti ulibe membala kadi umalimva kuwawa dziko lino koposa, moti makolo anthu ambiriwa amene sanaphunzirewa ambiriwa analibe ma kadi oti mkumayenda nawo. 2.Ukakhala kuti ulibe ndalama womungulira mkazi wako chitenje cha MCP umamangidwa moyo wonse kundende 3.Ukakhala kuti wagwiritsa ntchito news paper ngati kupita nawo ku chimbuzi yoti anajambulapo kamuzu ndiye kuti iweyo amakapatsira ngona 4.Akakuwona kuti iweyo ukufuna kuma yakhulayakhula nawo zosephana ndi kamuzu amakulowetsa mfuno mkamwa kapena kumatako mkukuwombera. 5.A peleniya amantha kungobwera mudzi mkuyamba kumenya wanthu komanso kuwalanda zinthu zawo ngati ngombe,chimanga,nkhuku,ndizina wosalakwa. 6.Tikuti nyimbo chabe maka inja amati afemu ukankhala wayimva yikuyimbidwa pawayilesi kaya ukutsekula mimba ukuyenera uziwonongere pompo koma usayende ukangoyenda ndiwe woukira wakulichete umenewo. 7.Kunalibe kuti wina atsutsa kanthu ukatsutsa umangosowa mosadziwika bwino,ukakhala ndi TV kapena ngalimoto umachita kumawonera kapena kukwera mwacheucheu zinali za Kamuzu yekha zimenezi. Eish misozi ikufuna kuyamba mmasomu zinazo pitirizani zikundivetsa chisoni.Mukuwona ngati bwezi FB ataloreza ku Malawi kuno??kkkk
Posted on: Sat, 17 Jan 2015 18:46:02 +0000

Trending Topics



style="min-height:30px;">
The goodwill and euphoria over the highly successful Manufacturing
It makes me incredibly disappointed and offended when ignorant

Recently Viewed Topics




© 2015