KULEMBESA MAKOPONI MFUMU: Alangizi afuna ayambe kulembera, - TopicsExpress



          

KULEMBESA MAKOPONI MFUMU: Alangizi afuna ayambe kulembera, pyalonga alangizi athu ba Boloma panavunjo? BONJESI: Ine ndivunjembo. ANTHU: Uuuuh ba Bonjesi khalanikwene pantchi, alangizi adembuka kale, ndie funa muwachedwese pontho basi. ALANGIZI: Vunjani. BONJESI: Anangofe penu ndi jeje penu, makomponi nee timbalembuwambooo tai. Chaka na chaka asalembuwa anthuache ngokhokhaoo. Kudya msolo wa mphende nkhupitisilana, ulendouno mutilembembo. Adyele boma okhokhaoo okhokhaoo, ifembo?
Posted on: Wed, 11 Sep 2013 03:50:11 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015