Koma Akazi aku Malawi omwe akukhala ku South Afrika amanyoza - TopicsExpress



          

Koma Akazi aku Malawi omwe akukhala ku South Afrika amanyoza bwanji. . . . Ati, amuna aku Malawi ngosasamba. sadziwa life. amangonunkha mkamwa. kwao mkunyera mmadzi, nyau, vimbuza ndi chasi zina. ku Malawi kuli madeya okhaokha. amuna eni eni ali ku CAPE TOWN, GAUTENG etc. kukwatiwa ndi mamuna wa ku MALAWI mkuzisakira umphawi ndi manda. mamuna ozindikira amakhala ku RSA . . tikatulutsa chibaluwa adziti ndine wa mkamwa, ndimatukwana. ayiwala kuti anabadwira ku MALAWI bambo wawo alinso ku MALAWI komanso ndi mMALAWI. anandiyankhulitsa pa mphepete ndithu
Posted on: Fri, 08 Nov 2013 21:06:15 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015