Koma jonzi ndi more! Kaya idzatheka.... Eeeh eh mkazi wadandaula - TopicsExpress



          

Koma jonzi ndi more! Kaya idzatheka.... Eeeh eh mkazi wadandaula uyu.... Amene mumawadziwa AMAPATSA MAKWESA ngati ali amzanu tawalangizani ku joniko kuti zomunyoza mkazi kuti hule akakukanani kumalawi kuno zimenezo zinatha. Mkazi akakana amuna akumalawi kuno jst move on wt their lives osati kumalemba pa fb kuti hule.mumuuzexo kuti ngati mkutheka apangeko improve chingerezi chakecho. Ma report akuti a MAKWESA anapita kujoni atangolakwa JC. Nkhani ngati izi zikuchulukira. Amalawi amene muli jonzi kodi sizingatheke kubwera kaye kumalawi kuno kuzaphuzira kenaka nkubweleraso?
Posted on: Wed, 31 Jul 2013 10:15:50 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015