Ku Tanzania tafikako moti nkhani yoti boma la Tanzania layika - TopicsExpress



          

Ku Tanzania tafikako moti nkhani yoti boma la Tanzania layika akasinja kumphepete a nyanja imene kwa iwo akuti lake nyasa ndi nkhambakamwa chabe akutchukitsa ndi ma media houses mumadziwa pa campaign one of the incumbent president manifesto was to fight to take half of the lake so that they can have authority over it ie buy vessels to be used for transport among those living along the lake. Ndiye ngati president mwamusankha ndiye akulemphera kukwanilitsa manifesto yake a tolankhani amayankhulatu, so this is what is happening ku Tanzania. Boma la Tanzania likuwopanso kuti litachita zamtopola Malawi ndiyowopsya kwambiri KING AFRICAN RIFLES as our solder are titled. The situation we have is a cold war as the mediation is still in progress to sort out the conflict.
Posted on: Wed, 19 Jun 2013 15:40:37 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015