LEADERSHIP AND EDUCATION IS VERY IS NT THE SAME .Ndaonela malawi - TopicsExpress



          

LEADERSHIP AND EDUCATION IS VERY IS NT THE SAME .Ndaonela malawi walero manyazi bwa? Minister of finance anabadwila kumalawi kmano anakulira ndikukalambila kunja,2 peter mutharika anabadwila kumalawi kukula ndikukalambila kunja,kungobwela okalambakalamba kale ,okutha kale kusonyedza kuti kaunjikayo ndiamene timakonda?Mukusinthanso mapaspt kuwakwezanso,azungu mumati akutumani aja akukana kucita help ,ana anu alikunja kwazikolino saphunzila kuno thus y mitengo ku university mwakweza kale.Olo tilile simumva poti ndalama zoyendetsela ziko mulibe kma zogulira #UDF NDI MCP MULINAZO.Mwatikwana katundu angokwela masana aliwonse kwacha nayo ingogwa usiku uliwonseeeeeeeeeee kuipa kovotela anthu oti alibe amalume awo ndi alongo awo nkumenekoooo2
Posted on: Wed, 05 Nov 2014 07:03:20 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015