Ladies... Atsikana tayankhani.. Upeza mkazi ali pantchito - TopicsExpress



          

Ladies... Atsikana tayankhani.. Upeza mkazi ali pantchito yabwino ndipo amalandila over K100 000 salary pa mwezi pamene boyfriend wake amagwila ntchito yau labour ndipo amalandila K35 000 pamwezi koma upeza mwezi ukatha mkazi akumupempha guy dora kuti ndikufuna ndalama yaku salon koma chonsecho nayenso walandila salary yake yambili yomposa bf wakeyo x3... Kumakhala kusakhutitsidwa kapena kufuna kumkhaulitsa bf wakoyo?? :) K£rnel The
Posted on: Mon, 11 Aug 2014 20:49:23 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015