MALAWI DZIKO LANGA!! Ukafuna kulemba munthu ntchito ukuti - TopicsExpress



          

MALAWI DZIKO LANGA!! Ukafuna kulemba munthu ntchito ukuti degree plus 3 yrs exp ayi koma diploma plus 5 yrs exp ikafika pa MSCE ndie iii!! mavuto kwa ma lova ati tikaone panyumba pako kuti ukasowetsa tidzaone chogwira. Kufika pa nyumba akapeza ya ma udzu dziwa kuti ntchito palibe angoti tikuimbila foni mapeto ake ungomva kuti anthu analowa mfield sha!. Xool tidalipilidwa ndi achifundo. L Banda kunalembedwa
Posted on: Tue, 20 Jan 2015 17:02:54 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015