MALAWI PASSPORT Amalawi amzanga ma passport anakweza mitengo - TopicsExpress



          

MALAWI PASSPORT Amalawi amzanga ma passport anakweza mitengo nde inu amene muli mmaiko osiyanasiyana mukamabwera kuno kumudzi muzibwera okhozeka ndikwacha yodzapangisira passport ina..Umu ndimmene mitengo ya passport ilili,akweza ndi 320%... -Ordinary Passport yachoka pa MK15,100 yafika pa MK48,500..Iyi imatenga 20days kuti ituluke.. -Express type of Passport,,yachoka pa MK25,100 yafika pa MK58,500..Iyi imatenga 5days kuti ituluke.. -Emergency Passport,yachoka pa MK35,100 yafika pa MK85,500,iyi imatenga 2days kuti ituluke... -Diplomatic Passport,yachoka pa MK85,000 yafika pa MK300,000 iyi imatenga 5days kuti ituluke... -Service type of Passport,yachoka pa MK19,500 yafika pa MK55,500 iyi imatenga 5days kuti ituluke.... Zinthu pakadali pano sizili bwino pa nyasaland moti ndalama za kunja zayambanso kusowa moti mafuta a Diesel,Petro ndi Paraffin(DPP)akwezanso posachedwapa... Mitengo ya mapassportyi yayamba kugwira ntchito pa 01 November 2014 paja.. APA MUZINGOTCHONA BASI KULIBE ZABWINO KUNO KUMUDZI.....TINAVOTERA MAVUTO DDD AYEEEEEEE!!!!!! kkkkkkkkkkkkkkkkk
Posted on: Tue, 04 Nov 2014 07:16:11 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015