MALAWIANS OF GOODWILL SHOULD REVISE WHETHER WE STILL NEED CHIEFS - TopicsExpress



          

MALAWIANS OF GOODWILL SHOULD REVISE WHETHER WE STILL NEED CHIEFS IN THE MODERN ERA: kodi mafumu ku Malawi kuonetsa DYERA mopanda manyazi chonchiku bwanji? Kususuka ndi ndalama za boma chonchi nkona anthu saakumawapatsanso ulemu and their role has become more redudant and too primitive to say the least: 1) Kale anthu amenewa ndi amene amagulitsa anthu awo ku ukapolo kwa ma arabs, sold us to colonialists. Conniving with strangers, foreigners, to vanquish their own clans and generations (Betrayers of their own people). Amatha kugulitsa anyamata amphambu onse mmudzi in exchange for kalilole (mirror) basi? 2) kenako established dictatorship during the one party state, Illusive to their own people! 3) Pano ndiye ndi akawalala kuba ndi ma kuponi a fertilizer omwe. Koma amenewadi ofunika ntchito yawo kuyionanso ACHOTSEDWE CHIFUKWA ALOWA DYERA..... 4) Anali oyamba kumasokosa nkhani ya devaluation ali mbuli zenizeni pa nkhani ya economy ya dziko. Nkumati kanyama ka devaluation ndikoyipa (kuli Bingu), kenako asintha nkumati devaluation ndi yabwino (ndi mayi JB); 5) Muluzi ayimenso? akuti ife mafumu tagwirizana kuti ayimenso; 6) Bingu kumutchula kuti Ngwazi, zoona? 7) Akuti kukana democracy, nkumati multiparty ndi nkhondo. Maybe amaopa kuti they will be more pressure for them to be accountable to the people; 8) Kenako kumanena kuti Malawi watukuka ndiye tisinthe flag. Tiyike flag ya dzuwa la mphumphu? Zoona malawi watukuka? Pamsonkhano pompo nkumati kumudziku kulibe milatho, kulibe sukulu, chipatala, koma akuti Malawi watukuka? 9) Kumayankha nkhani ya ndege, akuti ndege siimafunika ndipo iwowo amafuna chimanga? Anthu saamadziwa chilichonse mbuli pa nkhani ya chuma cha boma; 10) Lero ndiye ali yavwi yavwi akuti kukapereka petition kuti president achotse ma civil servants amene ali pa sitiraka? Zoona? Koma iwowa amadziwa kuti employment contracts za ma civil servants zimayenda bwanji? AMENEWA NTCHITO YAWO OFUNIKA ITHE. THEY ARE BRINGING MORE CONFUSION TO THE MALAWI SOCIETY.
Posted on: Thu, 08 Jan 2015 08:13:33 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015