MBIRI YA MA PRESIDENT APACHIBALE . 1. Ku America, George W Bush - TopicsExpress



          

MBIRI YA MA PRESIDENT APACHIBALE . 1. Ku America, George W Bush Senior anakhalapo President Kenako mwana wake George Bush . 2. Ku DRC, Lawrent Kabila anakhala President kenako mwana wake Josephy Kabila . 3. Ku Kenya, Jomo Kenyatta anakhala President kenako Mwana wake Uhuru Kenyatta. Ndiye inu mukamati kuno ku Malawi ndizosatheka mukutanthauza chani? For the First time in Malawi: • Bingu anali President kenako mmbale wake Pitala akhalanso president 2014. Pali Mau?
Posted on: Mon, 26 Aug 2013 17:45:09 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015