MSLNSF yapeza kuti sabata yomwe ikuyamba mawa ikhala sabata - TopicsExpress



          

MSLNSF yapeza kuti sabata yomwe ikuyamba mawa ikhala sabata yowawitsa kwambiri ku akulu-akulu a bungwe la Fam kamba kakuti anthu mazana-mazana akufuna akulu-akulu a bungweli kuti atule pansi ma udindo awo. Walter Nyamilandu,pamene amamema anthu kuti amuvoterenso pa mpando wa President wa bungweri,adalonjeza kuti adzapezera chithandizo ku ma team a Big Bullets komanso Mighty Wanderers,adapeza Company ya Carlzberg Malawi yomwe idangopusitsa ma team awirira, Walter Nyamirandu adalonjezanso kuti akasankhidwa,adzaitengera Malawi ku World Cup koma njira zomwe adagwiritsa ntchito potenga Thom Saintfeit sizidapindulire Malawi,chowawitsa china chomwe chapweteka a Malawi maka awo okonda masewera a mpira ndikukanidwa kwa Sponsership ya ndalama zambirimbiri kuchokera ku Airtel ati kamba kakuti bungwe la Fam lidasainila pangano ndi company ya tnm kuti palibe amene adzabwelenso ku mpira wa Miyendo,airtel yangopeleka ndalamazi ku masewera a ntchembere mbaye. Malinga ndi kafukufuku, ena mwa anthu amene amayendetsa mpira ati bungwe la Fam limapondelezanso ma team amene alibe chithandizo pomatenga gawo lalikuru pa ndalama za pa gate, anthu akufuna kuti executive ya Fam itule pansi ma udindo ake, sabata ino kuli ntchito,ife tatchera makutu athu,tizikudziwitsani zimene zikuchitika..........@Andy (the undisputed)
Posted on: Sun, 08 Sep 2013 08:21:47 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015