MTONDO KU SUKULU Mphunzitsi : ana inu Ana : ana - TopicsExpress



          

MTONDO KU SUKULU Mphunzitsi : ana inu Ana : ana ifeeeeee! Mphunzitsi : lero aliyense atchule dziko lakunja lomwe adzapite akazakula Ana: teacher!!! Teacher!!! Mphunzitsi :Eeeee malizani tayakha Malizani: ine mmafuna nzapite ku south africa Mphunzitsi : good boy,,, wina!! Biliyati : Ine mmafuna ndizapite ku Ghana Mphunzitsi: good boy...wina!! Nyotso: ine sindizapita kunja ndizafera mmalawi momuno. Mphunzitsi : Aaah mbuzii yamwana chitsiru chachabechabe iwee,,, suzapita chifukwa chan?, Nyotso ; Inuyo amphunzisi mukazakula muzapita kutiko? Mphunzitsi : aaah mnakula kale. Nyotso : nde pano muli kutiko? Osapita kunja bwanj? Mphunzitsi : sindimafunako Nyotso : Aaaaaaaaa mbuziii ya mphunzitsi chitsiru chenichen ...galu wachabechabe,,. MAU AMODZI KWA NYOTSO.
Posted on: Fri, 28 Nov 2014 18:16:31 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015