Madamu ku school adawauza ana kuti:monday aliyense pobwera - TopicsExpress



          

Madamu ku school adawauza ana kuti:monday aliyense pobwera azabwere ndika word kachizungu opanda kutero azalandila Chibalo sono Dingase ataweluka mnjira adapeza anthu akukangana ndipo adamva kachizungu kotir u crazy?ndipo Dingase adasunga ka word ko.atafika kunyumba Dingase adapita kwa Neighbour kukaonela Video usiku ndipo iye ataona kuti anthu atalikira adayamba kuseweletsa DVD PLAYER mpaka adampezelera ndipo iwo adati.iwe ukupanga chani apa mxiiiii u r stupit neh?Dingase adapeza kachizungu kachiwiri apa,ndipo ayini ake aja atatopa kuonera Video ija mamuna adamutenga mkazi wake kupita kokagona nati;lets go my darlingDingase adapeza kachizungu kachitatu. Sono Lolemba lafika. Madamu; nthawi ya chizungu sopano. John: goes. Madamu: well done john khala pansi. Wina? Petro: be free. Madamu: aaah wina? Sifati: never change. Madamu: wina? Dingase: r u crazy? Madamu: iwe Dingase ine!??? Dingase: u r stupit! Madamu: iwe Dingase mpaka pamenepo, tiye kwa Head master basi. Dingase: lets go my Darling. Kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk #MANTEMBO
Posted on: Sun, 27 Oct 2013 19:05:31 +0000

Trending Topics



iv class="sttext" style="margin-left:0px; min-height:30px;"> Sehe nur Ich den Widerspruch in sich??? 11.04.2013 "Wir fördern

Recently Viewed Topics




© 2015