Mafumu, senior chiefs, ali yakali yakali mtauni ya blantyre ndi - TopicsExpress



          

Mafumu, senior chiefs, ali yakali yakali mtauni ya blantyre ndi Lilongwe kukakamiza boma kuti lichotse ntchito anthu onse omwe akupanga strike. Funso mkumati wawathirira fuel kapena kuwapatsa transport kuti achoke ku chitipa, nsanje, mchinji, nkhotakota mkufika mtauni ndani ? Si bwampini mutharika yemweyu ? Chifukwa chani kumemeza mafumu kuti awukire anthu ake pokakamiza boma kamba kowapatsa allowance ? Shame on DPP illegal rigging government.
Posted on: Wed, 07 Jan 2015 06:43:18 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015