Malawi Freedom Network (MFN) wrote: ASILAMU AGAGADA NDUNA ZA PP - TopicsExpress



          

Malawi Freedom Network (MFN) wrote: ASILAMU AGAGADA NDUNA ZA PP KU MANGOCHI Nduna za boma la mayi JB, Ralph Joma ndi Ibrahim matola ndi ma body guard awo amenyedwa lero pa mzikiti wa Sub Mosque ku Mangochi. Ndiponso atolankhani a MBC TV amenyedwa akuti pojambula anzathu achisilamuwa pa Mosque mopanda chilolezo. Asilamuwa ati ndi okwiya kwambili ndi mchitidwe wa JB ndi Uladi mussa omanka natukwana mmisonkhano pog...
Posted on: Sat, 24 Aug 2013 16:53:52 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015