Malawi opposition have failed miserable coz of greedy and power - TopicsExpress



          

Malawi opposition have failed miserable coz of greedy and power hungry, pa chichewa pali mawu mukhale ogwirizana ngati mtolo wankhuni wina sazakuthyolani koma mukakhala kankhuni pa nokha muzathyoledwa mosavuta, Joyce Banda pa 21 may awina migolo migolo ife ku opposition tizizangolira kuti boma labera mavoti, kachipani kanu kakangono konyamulira mu chisakha kangatenge boma? Day dreaming ndithu, 2014 yatilaka basi mwina tichalire kuzalimbana ndi Mayi Joyce Banda 2019, pano ndiye taimba ngoma yongambika
Posted on: Thu, 08 May 2014 09:50:02 +0000

Trending Topics



Recently Viewed Topics




© 2015