Malawians,does it occur to u that now dzikoli layambaso kuopsa?there is insecurity,pple r desperate in their own land,2 wks ago a woman ws shot by robbers kwa che musa,that chinese investor ws shot,ku inde bank kubedwa,ena jst last wk amafuna kukaba mu pples ya kandondo cornershop,thanks to that police office,sanatenge zambiri,nanga hw many cases of roberies and murders occir daily,zomwe sizimalembedwa mu news ndi kuulutsidwa mma wailesi?ku machinjiri akuba ndiye avuta,they r even breaking into houses at meal times,kuba zida za mmagalimoto ndiye ndi daily.kodi nduna responsible for security ilipo? Someone told me its uladi mussa,is he doing his job,apart from kuyenda mmisonkhano with the president nkumatukwana anthu? Anthu mukumawatenga mmisonkhano mwanumo,nids protection,their lives and properties nid to be protected,pliz pliz mr minister do your job.
Posted on: Wed, 14 Aug 2013 22:56:27 +0000