Matilda Church ndi nkachisi wa Mulungu musavalemo dinda dinda - TopicsExpress



          

Matilda Church ndi nkachisi wa Mulungu musavalemo dinda dinda plz!!! Mu church ndi mokatamanda Namalenga sizomangotembenukira side ya a zibambo or ya azimayi,,,,imvani ulalikiro, abusa akuti chani, akazi muwatsirira akatuluka panja. Zokhala day dreaming pamene abusa akulalikira nde zosagwirazo pempherani kaye mowa nthawi ina,,,inde ma blues awina nkhalamba yanu Lampard yachinya congrats koma zimenezo mukaganize panja! Ine wanga ndawutalikitsa wa ku church, ndikakhuture machimo!
Posted on: Sun, 24 Nov 2013 03:37:42 +0000

Trending Topics



ner. Someone to light a fire under
It’s the first Jazz In The Round of the year and were starting
Sashas Rain and Wind Cover for Baby Trend Stride Sport Single

Recently Viewed Topics




© 2015